Yemwe akufuna kudzayima nawo pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino, a Milward Tobias, wauza mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, kuti afunsire nzeru kwa anthu ena pa mmene ...